Obadiya 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwe sumayenera kunyadira pa tsiku limene mʼbale wako anakumana ndi tsoka,+Sumayenera kusangalala pa tsiku limene anthu a ku Yuda ankawonongedwa,+Sumayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene ankazunzika. Obadiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12 Tsiku la Yehova, ptsa. 112-113
12 Iwe sumayenera kunyadira pa tsiku limene mʼbale wako anakumana ndi tsoka,+Sumayenera kusangalala pa tsiku limene anthu a ku Yuda ankawonongedwa,+Sumayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene ankazunzika.