13 Iwe sumayenera kulowa mumzinda wa anthu anga pa tsiku limene anakumana ndi tsoka.+
Sumayenera kunyadira pamene mʼbale wako ankavutika pa tsiku limene anakumana ndi tsoka.
Ndipo sumayeneranso kutenga chuma chake pa tsiku limene anakumana ndi tsoka.+