Obadiya 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwe sumayenera kuima panjira kuti uzipha anthu ake amene akuthawa.+Sumayeneranso kugwira anthu ake amene apulumuka nʼkuwapereka kwa adani awo pa tsiku limene ankazunzika.+
14 Iwe sumayenera kuima panjira kuti uzipha anthu ake amene akuthawa.+Sumayeneranso kugwira anthu ake amene apulumuka nʼkuwapereka kwa adani awo pa tsiku limene ankazunzika.+