Obadiya 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku la Yehova limene adzalange mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Zimene wachitira mʼbale wako, iwenso adzakuchitira zomwezo.+ Zimene unachitira anthu ena zidzakubwerera pamutu pako.
15 Tsiku la Yehova limene adzalange mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Zimene wachitira mʼbale wako, iwenso adzakuchitira zomwezo.+ Zimene unachitira anthu ena zidzakubwerera pamutu pako.