Obadiya 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mmene wamwera vinyo paphiri langa loyera,Ndi mmenenso mitundu ina yonse ya anthu izidzamwera mkwiyo wanga nthawi zonse.+ Iwo adzamwa ndi kugugudiza mkwiyo wanga,Ndipo zidzakhala ngati sanakhalepo nʼkomwe.
16 Mmene wamwera vinyo paphiri langa loyera,Ndi mmenenso mitundu ina yonse ya anthu izidzamwera mkwiyo wanga nthawi zonse.+ Iwo adzamwa ndi kugugudiza mkwiyo wanga,Ndipo zidzakhala ngati sanakhalepo nʼkomwe.