Yona 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno anayamba kuuzana kuti: “Tiyeni tichite maere+ kuti tidziwe amene wachititsa kuti tsokali litigwere.” Choncho anachitadi maere ndipo maerewo anagwera Yona.+ Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:7 Tsanzirani, tsa. 111 Nsanja ya Olonda,1/1/2009, tsa. 27
7 Ndiyeno anayamba kuuzana kuti: “Tiyeni tichite maere+ kuti tidziwe amene wachititsa kuti tsokali litigwere.” Choncho anachitadi maere ndipo maerewo anagwera Yona.+