Yona 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anayankha kuti: “Ndine Mheberi ndipo ndimaopa* Yehova Mulungu wakumwamba, amene anapanga nyanja ndi mtunda.”
9 Iye anayankha kuti: “Ndine Mheberi ndipo ndimaopa* Yehova Mulungu wakumwamba, amene anapanga nyanja ndi mtunda.”