Yona 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati: “Nditavutika kwambiri ndinaitana inu Yehova ndipo munandiyankha.+ Ndinafuula kupempha thandizo ndili mʼManda* akuya,+ Ndipo inu munamva mawu anga. Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, ptsa. 25-264/15/1989, tsa. 31 Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 85
2 Iye anati: “Nditavutika kwambiri ndinaitana inu Yehova ndipo munandiyankha.+ Ndinafuula kupempha thandizo ndili mʼManda* akuya,+ Ndipo inu munamva mawu anga.