Yona 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndinamira mpaka mʼmunsi mwenimweni mwa mapiri. Zotsekera za dziko lapansi zinayamba kunditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale. Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa mʼdzenje ndili wamoyo.+ Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:6 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, tsa. 26
6 Ndinamira mpaka mʼmunsi mwenimweni mwa mapiri. Zotsekera za dziko lapansi zinayamba kunditsekereza kuti ndikhale komweko mpaka kalekale. Koma inu Yehova Mulungu wanga, munanditulutsa mʼdzenje ndili wamoyo.+