Yona 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu. Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+ Yona Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Nsanja ya Olonda,5/15/1996, tsa. 26
9 Koma ine, ndidzakutamandani ndi kupereka nsembe kwa inu. Zimene ndalonjeza ndidzazikwaniritsa.+ Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.”+