-
Yona 3:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Uthengawo utafika kwa mfumu ya Nineve, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu nʼkuvula chovala chake chachifumu. Kenako inavala chiguduli nʼkukhala paphulusa.
-