-
Yona 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munthu aliyense komanso ziweto zivale chiguduli. Afuulire Mulungu kuchokera pansi pa mtima ndipo aliyense asiye zinthu zoipa komanso zachiwawa zimene amachita.
-