8 Dzuwa litatuluka, Mulungu anatumizanso mphepo yotentha yochokera kumʼmawa. Dzuwa linawotcha kwambiri Yona moti anangotsala pangʼono kukomoka. Choncho Yona anapempha mobwerezabwereza kuti angofa. Iye ankanena kuti: “Kuli bwino ndingofa kusiyana nʼkuti ndikhale ndi moyo.”+