Mika 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova analankhula ndi Mika*+ wa ku Morese mʼmasiku a Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda.+ Analankhula naye kudzera mʼmasomphenya ndipo anamuuza zokhudza Samariya ndi Yerusalemu kuti: Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:1 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 27
1 Yehova analankhula ndi Mika*+ wa ku Morese mʼmasiku a Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda.+ Analankhula naye kudzera mʼmasomphenya ndipo anamuuza zokhudza Samariya ndi Yerusalemu kuti: