Mika 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tamverani anthu nonsenu! Mvetsera mwatcheru iwe dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo.Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa akhale mboni yokutsutsani,+Yehova akutsutseni ali mʼkachisi wake woyera. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 11
2 “Tamverani anthu nonsenu! Mvetsera mwatcheru iwe dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo.Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa akhale mboni yokutsutsani,+Yehova akutsutseni ali mʼkachisi wake woyera.