Mika 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mapiri adzasungunuka kumapazi ake,+Ndipo zigwa zidzagawanika,Ngati phula losungunuka ndi moto.Ndipo zidzayenda ngati madzi othiridwa pamalo otsetsereka. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Tsiku la Yehova, ptsa. 31-32 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 11
4 Mapiri adzasungunuka kumapazi ake,+Ndipo zigwa zidzagawanika,Ngati phula losungunuka ndi moto.Ndipo zidzayenda ngati madzi othiridwa pamalo otsetsereka.