Mika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja,Malo oyenera kudzalapo mpesa.Miyala yake ndidzaiponya* mʼchigwa.Ndipo maziko ake ndidzawafukula nʼkuwasiya pamtunda. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 27
6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja,Malo oyenera kudzalapo mpesa.Miyala yake ndidzaiponya* mʼchigwa.Ndipo maziko ake ndidzawafukula nʼkuwasiya pamtunda.