-
Mika 1:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Inu anthu a ku Safiri, tulukani mʼdziko lanu muli maliseche ndiponso mukuchititsa manyazi.
Anthu a ku Zaanana sanachoke mʼdziko lawo.
Ku Beti-ezeli kuzingomveka kulira kokhakokha ndipo anthu ake adzasiya kukuthandizani.
-