Mika 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muchotse tsitsi lonse ndipo mumete mpala chifukwa cha ana anu amene mumawakonda. Metani mpala ngati wa chiwombankhanga,Chifukwa chakuti ana anuwo atengedwa kupita kudziko lina.”+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:16 Nsanja ya Olonda,11/1/2007, tsa. 155/1/1989, tsa. 14
16 Muchotse tsitsi lonse ndipo mumete mpala chifukwa cha ana anu amene mumawakonda. Metani mpala ngati wa chiwombankhanga,Chifukwa chakuti ana anuwo atengedwa kupita kudziko lina.”+