Mika 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsoka kwa anthu amene amakonza chiwembu,Amene akagona pabedi pawo, amaganizira kuti achite zoipa. Ndipo mʼmawa kukacha, amazichitadi.Chifukwa ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:1 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 12
2 “Tsoka kwa anthu amene amakonza chiwembu,Amene akagona pabedi pawo, amaganizira kuti achite zoipa. Ndipo mʼmawa kukacha, amazichitadi.Chifukwa ali ndi mphamvu zochitira zimenezo.+