Mika 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalakalaka minda ya anthu ena ndipo amaitenga.+Amalakalakanso nyumba za anthu ena nʼkuzitenga.Amatenga mwachinyengo nyumba ya munthu,+Ndipo amatenganso cholowa cha munthu. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 12
2 Iwo amalakalaka minda ya anthu ena ndipo amaitenga.+Amalakalakanso nyumba za anthu ena nʼkuzitenga.Amatenga mwachinyengo nyumba ya munthu,+Ndipo amatenganso cholowa cha munthu.