Mika 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yehova wanena kuti: ‘Ndikukonza zobweretsa tsoka+ pa banja ili, tsoka limene simudzatha kulithawa.+ Anthu inu simudzayendanso modzikuza+ chifukwa idzakhala nthawi ya tsoka.+
3 Choncho Yehova wanena kuti: ‘Ndikukonza zobweretsa tsoka+ pa banja ili, tsoka limene simudzatha kulithawa.+ Anthu inu simudzayendanso modzikuza+ chifukwa idzakhala nthawi ya tsoka.+