-
Mika 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Inu a mʼnyumba ya Yakobo, kodi mukunena kuti:
“Kodi mzimu wa Yehova sukuleza mtima?
Kodi zochita zake ndi zimenezi?”
Kodi mawu anga sapindulitsa anthu owongoka mtima?
-