Mika 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nyamukani muzipita, chifukwa malowa si opumulirako. Popeza dzikoli ndi lodetsedwa+ liwonongedwa, ndipo liwonongedwa koopsa.+
10 Nyamukani muzipita, chifukwa malowa si opumulirako. Popeza dzikoli ndi lodetsedwa+ liwonongedwa, ndipo liwonongedwa koopsa.+