Mika 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Munthu akatsatira zinthu zopanda pake ndi zachinyengo nʼkunena bodza lakuti: “Ndidzakulalikirani zokhudza vinyo ndi chakumwa choledzeretsa,” Adzangokhala mlaliki wa anthu awa.+
11 Munthu akatsatira zinthu zopanda pake ndi zachinyengo nʼkunena bodza lakuti: “Ndidzakulalikirani zokhudza vinyo ndi chakumwa choledzeretsa,” Adzangokhala mlaliki wa anthu awa.+