Mika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithu ndidzasonkhanitsa mbadwa zonse za Yakobo.Ndidzasonkhanitsa Aisiraeli otsala.+ Ndidzawabweretsa pamalo amodzi ngati gulu la nkhosa mʼkhola,Komanso ngati gulu la ziweto pamalo amsipu.+Kumeneko kudzakhala phokoso la anthu.’+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Nsanja ya Olonda,11/1/2007, tsa. 158/15/2003, ptsa. 12-135/1/1989, tsa. 14
12 Ndithu ndidzasonkhanitsa mbadwa zonse za Yakobo.Ndidzasonkhanitsa Aisiraeli otsala.+ Ndidzawabweretsa pamalo amodzi ngati gulu la nkhosa mʼkhola,Komanso ngati gulu la ziweto pamalo amsipu.+Kumeneko kudzakhala phokoso la anthu.’+