Mika 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mumadana ndi zinthu zabwino+ ndipo mumakonda zinthu zoipa.+Mumasenda khungu la anthu anga nʼkuchotsa mnofu pamafupa awo.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Tsiku la Yehova, ptsa. 77-78 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 145/1/1989, tsa. 14
2 Koma mumadana ndi zinthu zabwino+ ndipo mumakonda zinthu zoipa.+Mumasenda khungu la anthu anga nʼkuchotsa mnofu pamafupa awo.+