Mika 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumadyanso mnofu wa anthu anga,+Ndipo mumasenda khungu lawo.Mumaswa mafupa awo nʼkuwaphwanyaphwanya.+Ngati zinthu zimene zaphikidwa mumphika* komanso ngati nyama imene ili mumphika. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 145/1/1989, tsa. 14
3 Mumadyanso mnofu wa anthu anga,+Ndipo mumasenda khungu lawo.Mumaswa mafupa awo nʼkuwaphwanyaphwanya.+Ngati zinthu zimene zaphikidwa mumphika* komanso ngati nyama imene ili mumphika.