Mika 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Izi nʼzimene Yehova wanena zomwe zidzachitikire aneneri amene akusocheretsa anthu a mtundu wanga.+Amene amalengeza kuti ‘Mtendere!’+ kwinaku akuluma ndi mano awo.*+Koma munthu akapanda kuika chakudya mʼkamwa mwawo, amakonzekera zokamenyana naye:
5 Izi nʼzimene Yehova wanena zomwe zidzachitikire aneneri amene akusocheretsa anthu a mtundu wanga.+Amene amalengeza kuti ‘Mtendere!’+ kwinaku akuluma ndi mano awo.*+Koma munthu akapanda kuika chakudya mʼkamwa mwawo, amakonzekera zokamenyana naye: