Mika 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Usiku udzakufikirani,+ koma simudzaona masomphenya.+Kuzidzakhala mdima, koma inu simudzaloseranso. Aneneri amenewa dzuwa lidzawalowera.Ndipo mdima udzawagwera masanasana.+
6 ‘Usiku udzakufikirani,+ koma simudzaona masomphenya.+Kuzidzakhala mdima, koma inu simudzaloseranso. Aneneri amenewa dzuwa lidzawalowera.Ndipo mdima udzawagwera masanasana.+