-
Mika 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma ine ndapatsidwa mphamvu ndi mzimu wa Yehova.
Ndipo ndine wokonzeka kuchita chilungamo ndiponso kusonyeza mphamvu,
Kuti ndiuze mbadwa za Yakobo za kugalukira kwawo, komanso Isiraeli za tchimo lake.
-