Mika 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya YakoboKomanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+Amene mumadana ndi chilungamo ndiponso mumapotoza zinthu zonse zowongoka,+
9 Tamverani izi inu atsogoleri a nyumba ya YakoboKomanso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli,+Amene mumadana ndi chilungamo ndiponso mumapotoza zinthu zonse zowongoka,+