Mika 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho chifukwa cha anthu inu,Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja.+Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, ptsa. 16-17
12 Choncho chifukwa cha anthu inu,Ziyoni adzalimidwa ngati munda,Yerusalemu adzakhala mabwinja.+Ndipo phiri la nyumba* ya Mulungu lidzakhala ngati zitunda zamunkhalango.+