Mika 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo,Ndidzasonkhanitsa anthu amene ankayenda motsimphina.Ndidzasonkhanitsanso anthu amene anamwazikana,+Komanso anthu amene ndinawalanga.
6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo,Ndidzasonkhanitsa anthu amene ankayenda motsimphina.Ndidzasonkhanitsanso anthu amene anamwazikana,+Komanso anthu amene ndinawalanga.