-
Mika 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni udzamva ululu woopsa,
Ngati mkazi amene akubereka.
Chifukwa tsopano uchoka mʼtauni nʼkupita kukakhala kumudzi.
-