-
Mika 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Koma iwo sakudziwa maganizo a Yehova.
Iwo sakumvetsa cholinga chake.
Chifukwa adzawasonkhanitsa pamalo opunthira mbewu ngati mmene amasonkhanitsira tirigu amene angomumweta kumene.
-