Mika 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atsogoleriwo adzalanga dziko la Asuri ndi lupanga,+Komanso dziko la Nimurodi+ mʼnjira zake zonse zolowera mʼdzikolo. Wolamulirayo adzatipulumutsa kwa Asuri,+Asuriwo akadzangofika mʼdziko lathu nʼkuponda nthaka yathu. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2013, tsa. 208/15/1990, ptsa. 30-31
6 Atsogoleriwo adzalanga dziko la Asuri ndi lupanga,+Komanso dziko la Nimurodi+ mʼnjira zake zonse zolowera mʼdzikolo. Wolamulirayo adzatipulumutsa kwa Asuri,+Asuriwo akadzangofika mʼdziko lathu nʼkuponda nthaka yathu.