-
Mika 5:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mbadwa zotsala za Yakobo zidzakhala pakati pa mitundu yambiri ya anthu,
Ngati mame ochokera kwa Yehova.
Komanso ngati mvula yowaza imene ikugwa pazomera,
Yomwe sidalira munthu
Kapena kuyembekezera ana a anthu.
-