Mika 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi nditenge chiyani popita kwa Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba? Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu?Ndiponso ana a ngʼombe achaka chimodzi?+
6 Kodi nditenge chiyani popita kwa Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba? Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu?Ndiponso ana a ngʼombe achaka chimodzi?+