Mika 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mawu a Yehova akumveka mumzinda.Anthu anzeru zopindulitsa adzaopa dzina lanu. Mverani mawu a ndodo ndi a amene anaisankha.*+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2016, ptsa. 18-19 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 21
9 Mawu a Yehova akumveka mumzinda.Anthu anzeru zopindulitsa adzaopa dzina lanu. Mverani mawu a ndodo ndi a amene anaisankha.*+