Mika 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi mʼnyumba ya munthu woipa mukupezekabe chuma chopezedwa mopanda chilungamo?Ndiponso muyezo woperewera wa efa* umene ndi wonyansa? Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:10 Tsiku la Yehova, ptsa. 75-77 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 20
10 Kodi mʼnyumba ya munthu woipa mukupezekabe chuma chopezedwa mopanda chilungamo?Ndiponso muyezo woperewera wa efa* umene ndi wonyansa?