Mika 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mudzadzala mbewu, koma simudzakolola. Mudzaponda maolivi, koma simudzagwiritsa ntchito mafuta ake.Mudzapanga vinyo watsopano, koma simudzamwa vinyo.+
15 Mudzadzala mbewu, koma simudzakolola. Mudzaponda maolivi, koma simudzagwiritsa ntchito mafuta ake.Mudzapanga vinyo watsopano, koma simudzamwa vinyo.+