Mika 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita mwaukatswiri kwambiri.+Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso,Woweruza amauza anthu kuti amupatse chiphuphu.+Munthu wotchuka amauza anthu zimene akulakalaka,+Ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:3 Tsiku la Yehova, ptsa. 77-78 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 20
3 Manja awo amachita zoipa ndipo amazichita mwaukatswiri kwambiri.+Kalonga amalamula kuti amupatse mphatso,Woweruza amauza anthu kuti amupatse chiphuphu.+Munthu wotchuka amauza anthu zimene akulakalaka,+Ndipo onsewa amakonzera limodzi chiwembu.