Mika 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa mwana wamwamuna akunyoza bambo ake.Mwana wamkazi akutsutsana ndi mayi ake,+Ndipo mkazi wokwatiwa akutsutsana ndi apongozi ake aakazi.+Adani ake a munthu ndi anthu a mʼbanja lake.+ Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2013, tsa. 11
6 Chifukwa mwana wamwamuna akunyoza bambo ake.Mwana wamkazi akutsutsana ndi mayi ake,+Ndipo mkazi wokwatiwa akutsutsana ndi apongozi ake aakazi.+Adani ake a munthu ndi anthu a mʼbanja lake.+