Mika 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani wanga adzaonanso zimenezi,Ndipo manyazi adzagwira amene ankandinena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ Maso anga adzamuyangʼana. Iye adzapondedwapondedwa ngati matope amumsewu.
10 Mdani wanga adzaonanso zimenezi,Ndipo manyazi adzagwira amene ankandinena kuti: “Yehova Mulungu wako ali kuti?”+ Maso anga adzamuyangʼana. Iye adzapondedwapondedwa ngati matope amumsewu.