Mika 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Weta anthu ako ndi ndodo yako, gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako,+Zimene zinkakhala zokhazokha mʼnkhalango komanso pakati pa mitengo ya zipatso. Uzilole zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinkachitira kale. Mika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:14 Nsanja ya Olonda,8/15/2003, tsa. 245/1/1989, tsa. 16
14 Weta anthu ako ndi ndodo yako, gulu la nkhosa zomwe ndi cholowa chako,+Zimene zinkakhala zokhazokha mʼnkhalango komanso pakati pa mitengo ya zipatso. Uzilole zikadyere ku Basana ndi ku Giliyadi+ ngati mmene zinkachitira kale.