Mika 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+Ngati nyama zokwawa, adzatuluka akunjenjemera mʼmalo awo obisalamo. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akuchita mantha,Ndipo adzayamba kukuopani.”+
17 Adzanyambita fumbi ngati njoka.+Ngati nyama zokwawa, adzatuluka akunjenjemera mʼmalo awo obisalamo. Adzabwera kwa Yehova Mulungu akuchita mantha,Ndipo adzayamba kukuopani.”+