Nahumu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi Yehova mungamukonzere chiwembu chotani? Iye adzakufafanizani moti simudzakhalaponso. Sipadzakhalanso masautso.+ Nahumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, tsa. 9
9 Kodi Yehova mungamukonzere chiwembu chotani? Iye adzakufafanizani moti simudzakhalaponso. Sipadzakhalanso masautso.+