-
Nahumu 1:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iwo alukanalukana ngati minga,
Ndipo ali ngati anthu oledzera.
Koma adzawotchedwa ngati mapesi ouma.
-
10 Iwo alukanalukana ngati minga,
Ndipo ali ngati anthu oledzera.
Koma adzawotchedwa ngati mapesi ouma.