Nahumu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanena kuti: “Ngakhale kuti iwo anali ndi mphamvu zambiri komanso anali ambiri,Adzadulidwa ndipo sadzakhalaponso.* Ndakusautsa,* koma sindidzakusautsanso.
12 Yehova wanena kuti: “Ngakhale kuti iwo anali ndi mphamvu zambiri komanso anali ambiri,Adzadulidwa ndipo sadzakhalaponso.* Ndakusautsa,* koma sindidzakusautsanso.